Opani Mulungu, mpatseni ulemerero
7 ndi kunena ndi mau akuru, Opani Mulungu, mpatseni ulemerero; pakuti yafika nthawi ya ciweruziro cace; ndipo mlambireni iye amene analenga m'mwamba ndi mtunda ndi nyanja ndi akasupe amadzi, `Ndipo anatsata mngelo wina mnzace ndi kunena, Wagwa, wagwa, Babulo waukuru umene unamwetsako mitundu yonse ku vinyo wa mkwiyo wa cigololo cace.
Ndipo anawatsata mngelo wina, wacitatu, nanena ndi mau akuru, Ngati wina alambira ciromboco, ndi fane lace, nalandira lembapamphumi pace, kapena pa dzanja lace, iyenso adzamwako kuvinyo wa mkwiyo wa Mulungu, wokonzeka wosasanganiza m'cikho ca mkwiyo wace; ndipo adzazunzika ndi moto ndi sulfure pamaso pa angelo oyera mtima ndi pamaso pa Mwanawankhosa Osachotsera osaonjezera... Ndikufuna mulingilire mwakuya.... Kuti mukabwerako bwanji?
Mmene anthu akulimvera kukoma dzikoli? Funsani amene akulalikira akuuzani kuti muli zitonzo njiramu kutereko mukadzangoyamba kumva kuti nthawi ikanalipo mudzadziwe kuti mwadzibweza nokha dzaka 100 dzapitazo.